Mawu a M'munsi
a Patapita nthaŵi zinaonekeratu kuti Eliabu yemwe anali wokongolayo, analibe makhalidwe a mfumu yoyenera ya Israyeli. Pamene chimphona chachifilisiti, Goliati, chinaderera Aisrayeli kunkhondo, Eliabu ndi amuna ena achiisrayeli anachita mantha.—1 Samueli 17:11, 28-30.