Mawu a M'munsi
b Katswiri wina wa mbiri yakale, dzina lake Eusebius (yemwe anabadwa mu 260 C.E. n’kufa mu 340 C.E.) ananena kuti chisanafike chaka cha 66 C.E., “pothawa ziwembu zofuna kuwapha, atumwi anachoka ku Yudeya chifukwa moyo wawo unali pangozi. Koma pofuna kufalitsa uthenga wawo anapita m’chigawo chilichonse mwa mphamvu ya Khristu.”