Mawu a M'munsi c Kodi zimenezi zikutanthauza kuti munthu akasiya kuphunzira kapena kusonkhana ndi anthu a Yehova, ndiye kuti ndi wosafunika ndipo watayidwa ndi angelo? Ayi, si choncho. Ngati munthu akufunadi kubwerera kwa Yehova, khomo ndi lotseguka.—Mal. 3:7.