Mawu a M'munsi
a Nthawi zambiri Yesu ankadzitchula kuti “Mwana wa munthu.” (Mateyu 8:20) Mawu amenewa akusonyeza kuti pa nthawi imene anali padziko lapansi, iye anali munthu weniweni komanso kuti anali “mwana wa munthu” amene amatchulidwa mu ulosi wa m’Baibulo.—Danieli 7:13, 14.