Mawu a M'munsi
c Mawu achigiriki amene anawamasulira kuti “mdyerekezi” amatanthauza “munthu amene amanena mabodza oipitsa mbiri ya munthu wina.” Mdyerekezi ndi dzina linanso la Satana chifukwa chakuti ndi amene anayamba kunena mabodza oipitsa munthu wina.—Yoh. 8:44; Chiv. 12:9, 10.