Mawu a M'munsi
b Sitikudziwa ngati Akhristu ena achiheberi ankapereka nsembe pa Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo pambuyo pa Pentekosite mu 33 C.E. Koma ngati ankatero, ndiye kuti sankalemekeza nsembe ya Yesu. Chomwe tikudziwa n’chakuti Akhristu ena achiheberi anali kutsatirabe miyambo ina ya mu Chilamulo cha Mose.—Agal. 4:9-11.