Mawu a M'munsi
a Mu fanizoli, kufuula kuti, “Mkwati uja wafika!” kuli mu vesi 6 koma kufika kwake kwenikweni kuli mu vesi 10. Izi zikusonyeza kuti panadutsa nthawi kuchokera pamene anafuula kufika pamene anafikadi. M’masiku otsiriza ano, odzozedwa atcheru azindikira kuti Yesu akulamulira. Koma iwo ayenera kukhalabe maso mpaka iye atafika.