Mawu a M'munsi
a Mkhristu angasankhe kukhala ndi mfuti kuti azigwiritsa ntchito posaka kapena podziteteza ku nyama zolusa. Koma zingakhale bwino kusunga mfutiyo pamalo obisika ilibe zipolopolo kapena ili yomasula. M’mayiko amene amaletsa kukhala ndi mfuti kapena salola kukhala nayo chisawawa, Akhristu ayenera kutsatira malamulowo.—Aroma 13:1.