Mawu a M'munsi
a Pawebusaiti yathu pali nkhani zakuti “Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?” Nkhani zimenezi zikhoza kuthandiza ana ndi akulu omwe kuti azitha kumvetsa komanso kufotokoza mfundo za m’Baibulo. Mungazipeze pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA BAIBULO.