Mawu a M'munsi
a Anthu a Yehova akhala akuyembekezera Aramagedo kwa nthawi yaitali. Munkhaniyi tikambirana mafunso awa: Kodi Aramagedo n’chiyani? Kodi n’chiyani chidzachitike Aramagedo itatsala pang’ono kuyamba? Nanga tingatani kuti tikhalebe okhulupirika m’masiku otsirizawa?