Mawu a M'munsi
c Tingathandize anthu ena amene anafooka pophunzira nawo mitu ina ya m’buku lakuti Kodi Mungatani Kuti Mulungu Azikukondani? Kapenanso mitu ina m’buku lakuti Yandikirani kwa Yehova. Abale a m’Komiti ya Utumiki ya Mpingo ndi amene amasankha munthu woyenerera woti azichititsa phunziroli.