Mawu a M'munsi
a Akhristu satsatiranso Chilamulo cha Mose, komabe Chilamulochi chimatchula zinthu zina zimene tiyenera kuchita ndiponso zimene tiyenera kupewa. Kuphunzira mfundo zake kungatithandize kuti tizikonda anzathu komanso kusangalatsa Mulungu. Nkhaniyi ifotokoza mfundo zina zothandiza zimene tingaphunzire muchaputala 19 cha buku la Levitiko.