Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zoonera ndi Zomvetsera -Ezara Zithunzi komanso mavidiyo zopezeka pamalowa, zimakonzedwa patachitika kafukufuku wokwanira. Pa zinthu zingapo zomwe angakonze, nthawi zina okonza zithunzi ndi mavidiyowa angasankhe kuika chithunzi kapena vidiyo imodzi.