August Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya August 2016 Zitsanzo za Ulaliki August 1-7 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 87-91 Pitirizani Kukhala M’malo Otetezeka a Wam’mwambamwamba MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Tizithandiza Ophunzira Baibulo Athu Kuti Adzipereke Komanso Kubatizidwa August 8-14 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 92-101 Mukhoza Kumachitabe Zambiri Ngakhale Muli Okalamba August 15-21 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 102-105 Yehova Amakumbukira Kuti Ndife Fumbi August 22-28 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 106-109 ‘Muziyamikira Yehova’ August 29–September 4 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 110-118 ‘Kodi Yehova Ndidzamubwezera Chiyani?’ MOYO WATHU WA CHIKHRISTU Kuphunzitsa Choonadi MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tidzagwira Ntchito Yapadera Yogawira Nsanja ya Olonda mu September