-
Tetezani Dzina LanuNsanja ya Olonda—2000 | September 15
-
-
“Anthu sanyoza mbala ikaba, kuti ikhutitse mtima wake pomva njala,” akutikumbutsa motero. Komabe, “ikapezedwa idzabwezera kasanu ndi kaŵiri; idzapereka chuma chonse cha m’nyumba yake.” (Miyambo 6:30, 31) Mu Israyeli wakale, mbala inkafunikira kulipira ngakhale kuti zikatanthauza kupereka zonse zimene anali nazo.a Chotero n’koyeneratu kwambiri kupereka chilango kwa munthu wachigololo, yemwe alibiretu choŵiringula pa chomwe wachitacho!
-
-
Tetezani Dzina LanuNsanja ya Olonda—2000 | September 15
-
-
a Malinga ndi Chilamulo cha Mose, wakuba ankayenera kubwezera kuŵirikiza kawiri, kanayi, kapena kuŵirikiza kasanu. (Eksodo 22:1-4) Mawu akuti “kasanu ndi kaŵiri” mwachionekere akutanthauza chilango cha kalavula gaga, chomwe chingathe kukhala kuŵirikiza kambirimbiri zomwe anali atabazo.
-