-
Kodi Pali Munthu Amene Anaonapo Mulungu?Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
-
-
Masomphenya.
Mulungu ankaonekera kwa anthu kudzera m’masomphenya, kapena kuti zinthu zimene anthuwo ankaona m’maganizo mwawo. Mwachitsanzo, Baibulo likamanena kuti Mose ndi Aisiraeli “anaona Mulungu wa Isiraeli,” limatanthauza kuti “iwo anaona masomphenya a Mulungu woona.” (Ekisodo 24:9-11) Mofanana ndi zimenezi nthawi zina Baibulo limanena kuti aneneri ‘ankaona Yehova.’ (Yesaya 6:1; Danieli 7:9; Amosi 9:1) Nkhani zonsezi zikusonyezeratu kuti anthuwo sankaona Mulungu weniweni koma ankangoona masomphenya.—Yesaya 1:1; Danieli 7:2; Amosi 1:1.
-
-
Kodi Mulungu Ali ndi Mayina Angati?Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
-
-
Wamasiku Ambiri
Mulungu alibe chiyambi. Iye wakhala alipo kuyambira kalekale munthu aliyense komanso chinthu chilichonse zisanapangidwe.—Salimo 90:2.
-