-
Asuri Wankhalwe—Mphamvu Yaikulu ya Dziko YachiŵiriNsanja ya Olonda—1988 | February 15
-
-
Bukhu la Nahumu limatsegula ndi mawu awa: “Kugamula molimbana ndi Nineve”, likulu la Asuri. Nchifukwa ninji? Chifukwa, monga momwe mneneri Nahumu pambuyo pake akulongosolera, Nineve unali “mudzi wa mwazi . . . udzala nawo mabodza ndi zachifwamba.” (Nahumu 1:1; 3:1, NW) Kodi iye anali kunena monkitsa? Kutalitali!
-
-
Asuri Wankhalwe—Mphamvu Yaikulu ya Dziko YachiŵiriNsanja ya Olonda—1988 | February 15
-
-
Pamene Nineve anagwa, kusakazidwa kwake kunali kotheratu chakuti kwa zaka mazana malo ake anaiwalidwa. Osuliza ena amanyoza Baibulo, akumanena kuti mzinda umenewu sunakhalepo nkomwe. Koma iwo unakhalakodi! Unadzapezedwanso, ndipo zimene akatswiri odziŵa zofukulidwa pansi anapeza zinalidi zosangalatsa!
-