-
Mafunso Ochokera kwa OwerengaNsanja ya Olonda—2014 | November 15
-
-
Chochititsa chidwi n’chakuti lemba la Chivumbulutso 11:1, 2 limanenanso za kuyeza kachisi wauzimu. Chaputala 3 cha Malaki chimanenanso za kuyendera kachisi wauzimu komanso kumuyeretsa. (Mal. 3:1-4) Kuyendera kachisi ndi kumuyeretsa kunachitika kuyambira mu 1914 mpaka chakumayambiriro kwa 1919. Nthawiyi ikuimiridwa ndi masiku 1,260 (kapena kuti miyezi 42) kuphatikiza ndi masiku atatu ndi hafu otchulidwa m’chaputala 11 cha Chivumbulutso.
-