-
Mfundo Zazikulu za M’makalata Opita kwa Agalatiya, Aefeso, Afilipi, ndi AkoloseNsanja ya Olonda—2008 | August 15
-
-
6:2—Kodi “chilamulo cha Khristu” n’chiyani? Chilamulo chimenechi ndi zinthu zonse zimene Yesu anaphunzitsa komanso zimene analamula makamaka lamulo lakuti ‘tizikondana wina ndi mnzake.’—Yoh. 13:34.
-