-
N’chiyani Chingatithandize Kuti Tizisankha Zinthu Mwanzeru?Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
-
-
3. Muzitsatira mfundo za m’Baibulo
Kodi mfundo za m’Baibulo zingatithandize bwanji tikamasankha zochita? Onerani VIDIYO, kenako mukambirane mafunso otsatirawa.
Kodi Yehova anatipatsa mphatso yamtengo wapatali iti?
N’chifukwa chiyani Yehova anatipatsa mphatso imeneyi?
Kodi Yehova watipatsa chiyani pofuna kutithandiza kusankha zinthu mwanzeru?
Kuti muone chitsanzo cha mfundo ya m’Baibulo, werengani Aefeso 5:15, 16. Kenako mukambirane mmene ‘mungagwiritsire ntchito bwino nthawi yanu’ . . .
powerenga Baibulo tsiku lililonse.
kuti mukhale mwamuna kapena mkazi wabwino, kholo kapenanso mwana wabwino.
kuti muzichita nawo misonkhano yampingo.
-
-
Muzisankha Zosangalatsa Zomwe Sizingakhumudwitse YehovaMungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
-
-
2. N’chifukwa chiyani tifunika kusamala kuti tisamangokhalira kuchita zosangalatsa?
Ngakhale titasankha zosangalatsa zimene sizingakhumudwitse Yehova, tifunika kusamala kuti tisamangokhalira kuchita zosangalatsazo. Zili choncho chifukwa chakuti kupanda kusamala tingalephere kupeza nthawi yochitira zinthu zofunika kwambiri. Baibulo limatilimbikitsa kuti ‘tizigwiritsa ntchito bwino nthawi yathu.’—Werengani Aefeso 5:15, 16.
-
-
Muzisankha Zosangalatsa Zomwe Sizingakhumudwitse YehovaMungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
-
-
4. Muzigwiritsa ntchito nthawi yanu mwanzeru
Onerani VIDIYO, kenako mukambirane funso ili:
Ngakhale kuti m’bale wamuvidiyoyi sankaonera zinthu zoipa, kodi vuto lake linali lotani?
Werengani Afilipi 1:10, kenako mukambirane funso ili:
Kodi vesili lingatithandize bwanji kupewa kuthera nthawi yaitali pa zinthu zosangalatsa?
-