-
Mfundo Zazikulu za M’makalata Opita kwa Tito, Filemoni ndi AheberiNsanja ya Olonda—2008 | October 15
-
-
15, 16—Kodi n’chifukwa chiyani Paulo sanapemphe Filemoni kuti amasule Onesimo? Paulo ankafuna kungogwira ntchito yake ‘yolalikira za ufumu wa Mulungu, ndi kuphunzitsa za Ambuye Yesu Khristu’ basi. Motero, sanafune kulowerera m’nkhani zina, monga zokhudza ukapolo.—Mac. 28:31.
-
-
Mfundo Zazikulu za M’makalata Opita kwa Tito, Filemoni ndi AheberiNsanja ya Olonda—2008 | October 15
-
-
15, 16. Ngati zinthu sizikuyenda bwino pamoyo wathu tisamade nkhawa kwambiri. Zinthu zingathe kusintha monga zinakhalira kwa Onesimo.
-