B14-A
Miyezo ya Zinthu Ndiponso Malonda
Miyezo ya Zinthu Zamadzi
Kori (Mitsuko 10 / Mahini 60)
Malita 220 / Magaloni 58.1
Mtsuko (Mahini 6)
Malita 22 / Magaloni 5.81
Hini (Malogi 12)
Malita 3.67 / Mapainti 7.75
Logi (1⁄12 hini)
Malita 0.31 / Mapainti 0.66
Miyezo ya Zinthu Zomwe Si Zamadzi
Homeri (Kori imodzi / Maefa 10)
Malita 220
Efa (Maseya atatu / Maomeri 10)
Malita 22
Seya (Maomeri 31⁄3)
Malita 7.33
Omeri (Makabu 14⁄5)
Malita 2.2 / Makwati 2
Kabu
Malita 1.22 / Makwati 1.11
Kwati
Malita 1.08
Miyezo Yoyezera Mtunda
Bango lalitali (Mikono 6 yaitali)
Mamita 3.11 / Mafiti 10.2
Bango (Mikono 6)
Mamita 2.67 / Mafiti 8.75
Fatomu
Mamita 1.8 / Mafiti 6
Mkono umodzi (Zikhatho 7)
Masentimita 51.8 / Mainchesi 20.4
Mkono (Masipani awiri / Zikhatho 6)
Masentimita 44.5 / Mainchesi 17.5
Mkono waufupi
Masentimita 38 / Mainchesi 15
Sitadiya imodzi ya Chiroma 1⁄8 ya mailo ya Chiroma
= Mamita 185 / Mafiti 606.95
1 Mphipi imodzi ya chala (1⁄4 ya chikhatho)
Masentimita 1.85 / Mainchesi 0.73
2 Chikhatho (Mphipi ya zala 4)
Masentimita 7.4 / Mainchesi 2.9
3 Sipani (Zikhatho zitatu)
Masentimita 22.2 / Mainchesi 8.75