Masalimo
2 Mutamandeni chifukwa cha ntchito zake zamphamvu.+
Mutamandeni mogwirizana ndi ukulu wake wosaneneka.+
3 Mutamandeni mwa kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+
Mutamandeni ndi choimbira cha zingwe ndi zeze.+
Palibe Vidiyo.
Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.