Genesis 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tiye tipatukane. Ukhoza kutenga mbali iliyonse ya dzikoli. Iwe ukapita kumanzere, ine ndipita kumanja, koma iwe ukapita kumanja, ine ndipita kumanzere.”+ Miyambo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chiyambi cha mkangano chili ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.+ Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+ Aroma 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati ndi kotheka, khalani mwamtendere+ ndi anthu onse, monga mmene mungathere.
9 Tiye tipatukane. Ukhoza kutenga mbali iliyonse ya dzikoli. Iwe ukapita kumanzere, ine ndipita kumanja, koma iwe ukapita kumanja, ine ndipita kumanzere.”+
14 Chiyambi cha mkangano chili ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.+ Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+