Amosi 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu mukapereka nsembe zathunthu zopsereza,+ ine sindidzasangalala ndi nsembe zanuzo zoperekedwa ngati mphatso,+ ndipo sindidzayang’ana nsembe zanu zachiyanjano zanyama zonenepa.+
22 Inu mukapereka nsembe zathunthu zopsereza,+ ine sindidzasangalala ndi nsembe zanuzo zoperekedwa ngati mphatso,+ ndipo sindidzayang’ana nsembe zanu zachiyanjano zanyama zonenepa.+