Genesis 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero Yehova anati: “Kudandaula kokhumudwa chifukwa cha Sodomu ndi Gomora+ kwamveka kwambiri, ndipo tchimo lawo n’lalikulu kwambiri.+ 2 Mafumu 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ‘“Ndithu magazi+ a Naboti ndi magazi a ana ake+ amene ndawaona dzulo,” watero Yehova, “ndidzawabwezera+ pa iwe ndithu m’munda uwu,” Yehova watero.’ Choncho munyamule, umuponye m’mundamo mogwirizana ndi mawu a Yehova.”+ Yesaya 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala kuti adzaimbe mlandu anthu okhala m’dzikoli.+ Magazi amene dzikoli linakhetsa lidzawaonetsa poyera,+ ndipo silidzabisanso anthu amene linapha.”+ Aheberi 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi owaza,+ amene amalankhula m’njira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+
20 Chotero Yehova anati: “Kudandaula kokhumudwa chifukwa cha Sodomu ndi Gomora+ kwamveka kwambiri, ndipo tchimo lawo n’lalikulu kwambiri.+
26 ‘“Ndithu magazi+ a Naboti ndi magazi a ana ake+ amene ndawaona dzulo,” watero Yehova, “ndidzawabwezera+ pa iwe ndithu m’munda uwu,” Yehova watero.’ Choncho munyamule, umuponye m’mundamo mogwirizana ndi mawu a Yehova.”+
21 Pakuti taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala kuti adzaimbe mlandu anthu okhala m’dzikoli.+ Magazi amene dzikoli linakhetsa lidzawaonetsa poyera,+ ndipo silidzabisanso anthu amene linapha.”+
24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi owaza,+ amene amalankhula m’njira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+