2 Mafumu 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tikati, ‘Tiyeni tilowe mumzinda,’ tikafera momwemo chifukwa muli njala.+ Tikatinso tikhale pano, tifa. Ndiye tiyeni tikalowe mumsasa wa Asiriya. Akakatisiya ndi moyo, tikhala ndi moyo, koma akakatipha, chabwino tikafa.”+ Machitidwe 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Titalephera kumusintha maganizo, tinangovomereza ndi kunena kuti: “Chifuniro+ cha Yehova chichitike.”
4 Tikati, ‘Tiyeni tilowe mumzinda,’ tikafera momwemo chifukwa muli njala.+ Tikatinso tikhale pano, tifa. Ndiye tiyeni tikalowe mumsasa wa Asiriya. Akakatisiya ndi moyo, tikhala ndi moyo, koma akakatipha, chabwino tikafa.”+
14 Titalephera kumusintha maganizo, tinangovomereza ndi kunena kuti: “Chifuniro+ cha Yehova chichitike.”