-
Deuteronomo 21:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Pakuti ayenera kuvomereza kuti mwana wamwamuna wa mkazi wake wosakondedwayo ndiye woyamba kubadwa. Azivomereza mwa kum’patsa magawo awiri pa chilichonse chimene ali nacho,+ chifukwa mwanayo ndiye chiyambi cha mphamvu zake zobereka.+ Mwana ameneyo ndiye woyenera kulandira udindo wa mwana woyamba kubadwa.+
-