-
Yesaya 9:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Komabe mdima wake sudzakhala ngati wa pa nthawi imene dzikolo linali m’masautso, ngati kale pamene anthu ankanyoza dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafitali.+ Koma patsogolo pake anthu analilemekeza dzikolo,+ dera limene kuli njira ya m’mphepete mwa nyanja, m’chigawo cha Yorodano, ku Galileya kumene kunali kukhala anthu a mitundu ina.+
-