Levitiko 26:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Chotero ndidzakumbukira pangano langa limene ndinachita ndi Yakobo.+ Ndidzakumbukiranso pangano langa ndi Isaki+ komanso ndi Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo. Yesaya 54:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi a Nowa sadzadutsanso padziko lapansi,+ momwemonso ndalumbira kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+
42 Chotero ndidzakumbukira pangano langa limene ndinachita ndi Yakobo.+ Ndidzakumbukiranso pangano langa ndi Isaki+ komanso ndi Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo.
9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi a Nowa sadzadutsanso padziko lapansi,+ momwemonso ndalumbira kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+