Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake. 1 Akorinto 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwamuna sayenera kuphimba kumutu kwake, popeza iye ndi chifaniziro+ ndi ulemerero+ wa Mulungu, koma mkazi ndi ulemerero wa mwamuna.+ Akolose 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo muvale umunthu watsopano+ umene Mulungu amapereka, kutanthauza kuti mwa kudziwa zinthu molondola, muchititse umunthu wanu kukhala watsopano mogwirizana ndi chifaniziro+ cha Mulungu.
6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.
7 Mwamuna sayenera kuphimba kumutu kwake, popeza iye ndi chifaniziro+ ndi ulemerero+ wa Mulungu, koma mkazi ndi ulemerero wa mwamuna.+
10 ndipo muvale umunthu watsopano+ umene Mulungu amapereka, kutanthauza kuti mwa kudziwa zinthu molondola, muchititse umunthu wanu kukhala watsopano mogwirizana ndi chifaniziro+ cha Mulungu.