Yeremiya 50:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Yehova ananena mawu okhudza Babulo,+ dziko la Akasidi,+ kudzera mwa mneneri Yeremiya. Iye anati: 1 Petulo 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mayi* amene ali ku Babulo,+ wosankhidwa mwapadera ngati inuyo, komanso mwana wanga Maliko,+ akupereka moni.
13 Mayi* amene ali ku Babulo,+ wosankhidwa mwapadera ngati inuyo, komanso mwana wanga Maliko,+ akupereka moni.