Genesis 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno, mfumu ya ku Sodomu inapita kuchigwa cha Save, kapena kuti chigwa cha mfumu.+ Inapita kukakumana ndi Abulamu, pamene anali kubwera kuchokera kumene anakagonjetsa Kedorelaomere, limodzi ndi mafumu amene anali naye.
17 Ndiyeno, mfumu ya ku Sodomu inapita kuchigwa cha Save, kapena kuti chigwa cha mfumu.+ Inapita kukakumana ndi Abulamu, pamene anali kubwera kuchokera kumene anakagonjetsa Kedorelaomere, limodzi ndi mafumu amene anali naye.