Genesis 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako Mulungu anati: “Tiyeni+ tipange munthu m’chifaniziro chathu,+ kuti akhale wofanana nafe.+ Ayang’anire nsomba zam’nyanja ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga, komanso nyama zoweta. Ayang’anirenso dziko lonse lapansi ndi nyama zonse zokwawa padziko lapansi.”+ Salimo 139:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzakutamandani chifukwa munandipanga modabwitsa ndipo zimenezi zimandichititsa mantha.+Ntchito zanu ndi zodabwitsa,+Ndipo ine ndimadziwa bwino zimenezi.+ Aroma 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu iwe!+ Iweyo ndiwe ndani kuti uziyankhana ndi Mulungu?+ Kodi chinthu choumbidwa chinganene kwa munthu amene anachiumba kuti, “Unandipangiranji motere?”+
26 Kenako Mulungu anati: “Tiyeni+ tipange munthu m’chifaniziro chathu,+ kuti akhale wofanana nafe.+ Ayang’anire nsomba zam’nyanja ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga, komanso nyama zoweta. Ayang’anirenso dziko lonse lapansi ndi nyama zonse zokwawa padziko lapansi.”+
14 Ndidzakutamandani chifukwa munandipanga modabwitsa ndipo zimenezi zimandichititsa mantha.+Ntchito zanu ndi zodabwitsa,+Ndipo ine ndimadziwa bwino zimenezi.+
20 Munthu iwe!+ Iweyo ndiwe ndani kuti uziyankhana ndi Mulungu?+ Kodi chinthu choumbidwa chinganene kwa munthu amene anachiumba kuti, “Unandipangiranji motere?”+