Ekisodo 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Pokumbukira kuti muyenera kusunga tsiku la sabata ndi kuliona kukhala lopatulika,+ Levitiko 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Muzisunga masabata anga+ ndipo muziopa malo anga opatulika.+ Ine ndine Yehova. Akolose 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 pakuti zinthu zimenezo ndi mthunzi+ wa zimene zinali kubwera, koma zenizeni+ zake zili mwa Khristu.+
17 pakuti zinthu zimenezo ndi mthunzi+ wa zimene zinali kubwera, koma zenizeni+ zake zili mwa Khristu.+