Salimo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+ Salimo 94:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova sadzataya anthu ake,+Kapena kusiya cholowa chake.+
12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+