Ekisodo 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ine ndilola Aiguputo kuumitsa mitima yawo,+ kuti atsatire Aisiraeli panyanjapo, kutinso ndipezerepo ulemerero mwa kugonjetsa Farao, magulu ake onse ankhondo, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.+ Miyambo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova anapanga chilichonse n’cholinga,+ ndipo ngakhale woipa anamusungira tsiku loipa.+
17 Koma ine ndilola Aiguputo kuumitsa mitima yawo,+ kuti atsatire Aisiraeli panyanjapo, kutinso ndipezerepo ulemerero mwa kugonjetsa Farao, magulu ake onse ankhondo, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.+