Ekisodo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho anawaikira akulu owayang’anira pa ntchito yawo yaukapolo, kuti aziwanyamulitsa katundu mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.* Ekisodo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+ Machitidwe 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tsopano pamene anakwanitsa zaka 40 zakubadwa, anaganiza zokayendera abale ake, ana a Isiraeli.+
11 Choncho anawaikira akulu owayang’anira pa ntchito yawo yaukapolo, kuti aziwanyamulitsa katundu mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.*
7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+