-
Nehemiya 9:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Chifukwa chochita zimenezi, munawapereka m’manja mwa adani awo+ amene anapitiriza kuwasautsa.+ Koma akakumana ndi nsautso, anali kukulirirani,+ ndipo inu munali kumva muli kumwambako.+ Chifukwa cha chifundo chanu chachikulu,+ munali kuwapatsa owapulumutsa+ amene anali kuwalanditsa m’manja mwa adani awo.+
-