Ekisodo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli, 1 Mafumu 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho anadzuka ndipo anadya ndi kumwa. Atatero, anapeza mphamvu zokwanira moti anatha kuyenda masiku 40,+ usana ndi usiku, mpaka kukafika kuphiri la Mulungu woona la Horebe.+ Malaki 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Anthu inu kumbukirani chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi zigamulo zimene ndinam’patsa ku Horebe zokhudza Aisiraeli onse.+
6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli,
8 Choncho anadzuka ndipo anadya ndi kumwa. Atatero, anapeza mphamvu zokwanira moti anatha kuyenda masiku 40,+ usana ndi usiku, mpaka kukafika kuphiri la Mulungu woona la Horebe.+
4 “Anthu inu kumbukirani chilamulo cha Mose mtumiki wanga. Kumbukirani malamulo ndi zigamulo zimene ndinam’patsa ku Horebe zokhudza Aisiraeli onse.+