Levitiko 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati wansembe, wodzozedwa,+ wachita tchimo+ limene lapalamulitsa anthu onse, azipereka kwa Yehova ng’ombe yaing’ono yamphongo yopanda chilema monga nsembe yamachimo chifukwa cha tchimo lakelo.+
3 “‘Ngati wansembe, wodzozedwa,+ wachita tchimo+ limene lapalamulitsa anthu onse, azipereka kwa Yehova ng’ombe yaing’ono yamphongo yopanda chilema monga nsembe yamachimo chifukwa cha tchimo lakelo.+