Ekisodo 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako utenge mafuta odzozera+ ndi kuwathira pamutu pake ndi kum’dzoza.+ Ekisodo 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Udzoze Aroni+ ndi ana ake,+ ndipo uwayeretse kuti atumikire monga ansembe anga.+ Ekisodo 40:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ukatero, udzaveke Aroni zovala zopatulika,+ kenako um’dzoze+ ndi kumuyeretsa kuti atumikire monga wansembe wanga. Levitiko 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Ndipo mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, wodzozedwa mafuta pamutu pake,+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti avale zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala+ ndipo asang’ambe zovala zake.+ Salimo 133:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu,+Amene akutsikira kundevu,Ndevu za Aroni,+Amenenso akuyenderera mpaka m’khosi la zovala zake.+ Machitidwe 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nkhani yake inali yonena za Yesu wa ku Nazareti, kuti Mulungu anamudzoza ndi mzimu woyera+ ndi mphamvu. Ndiponso kuti popeza Mulungu anali naye,+ anayendayenda m’dziko, n’kumachita zabwino ndi kuchiritsa onse osautsidwa ndi Mdyerekezi.+
13 Ukatero, udzaveke Aroni zovala zopatulika,+ kenako um’dzoze+ ndi kumuyeretsa kuti atumikire monga wansembe wanga.
10 “‘Ndipo mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, wodzozedwa mafuta pamutu pake,+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti avale zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala+ ndipo asang’ambe zovala zake.+
2 Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu,+Amene akutsikira kundevu,Ndevu za Aroni,+Amenenso akuyenderera mpaka m’khosi la zovala zake.+
38 Nkhani yake inali yonena za Yesu wa ku Nazareti, kuti Mulungu anamudzoza ndi mzimu woyera+ ndi mphamvu. Ndiponso kuti popeza Mulungu anali naye,+ anayendayenda m’dziko, n’kumachita zabwino ndi kuchiritsa onse osautsidwa ndi Mdyerekezi.+