Levitiko 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Musamadye mafuta kapena magazi+ alionse. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale,* kulikonse kumene mungakhale.’” Levitiko 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu akapita kosaka nyama, ndipo wapha nyama kapena mbalame yololeka kudya, azithira magazi ake pansi+ ndi kuwafotsera ndi dothi.+ Deuteronomo 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ungokhala wotsimikiza mtima kwambiri kusadya magazi,+ chifukwa magazi ndiwo moyo,+ ndipo suyenera kudya nyama pamodzi ndi moyo wake. Machitidwe 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma tiyeni tiwalembere kuti apewe zinthu zoipitsidwa ndi mafano,+ dama,*+ zopotola,+ ndi magazi.+ Machitidwe 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma kwa okhulupirira ochokera mwa anthu a mitundu inawo, tinawatumizira chigamulo chathu chakuti apewe zoperekedwa nsembe kwa mafano+ komanso magazi,+ zopotola,+ ndi dama.”+
17 “‘Musamadye mafuta kapena magazi+ alionse. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale,* kulikonse kumene mungakhale.’”
13 “‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu akapita kosaka nyama, ndipo wapha nyama kapena mbalame yololeka kudya, azithira magazi ake pansi+ ndi kuwafotsera ndi dothi.+
23 Koma ungokhala wotsimikiza mtima kwambiri kusadya magazi,+ chifukwa magazi ndiwo moyo,+ ndipo suyenera kudya nyama pamodzi ndi moyo wake.
20 Koma tiyeni tiwalembere kuti apewe zinthu zoipitsidwa ndi mafano,+ dama,*+ zopotola,+ ndi magazi.+
25 Koma kwa okhulupirira ochokera mwa anthu a mitundu inawo, tinawatumizira chigamulo chathu chakuti apewe zoperekedwa nsembe kwa mafano+ komanso magazi,+ zopotola,+ ndi dama.”+