1 Akorinto 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+ Akolose 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano. 1 Atesalonika 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu akufuna kuti mukhale oyera+ mwa kupewa dama.*+
9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+
5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano.