Numeri 1:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Ana a Isiraeli anachita zonse monga mmene Yehova analamulira Mose. Anachitadi momwemo.+