Levitiko 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kapena chilichonse chimene angalumbirire monama. Azibweza+ chinthucho ndi kuwonjezerapo limodzi mwa magawo ake asanu. Iye azibweza zimenezi kwa mwiniwake, tsiku limene kulakwa kwake kwatsimikizidwa.
5 kapena chilichonse chimene angalumbirire monama. Azibweza+ chinthucho ndi kuwonjezerapo limodzi mwa magawo ake asanu. Iye azibweza zimenezi kwa mwiniwake, tsiku limene kulakwa kwake kwatsimikizidwa.