Salimo 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikomereni mtima ine mtumiki wanu.+Ndipulumutseni mwa kukoma mtima kwanu kosatha.+ Salimo 67:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Mulungu adzatiyanja ndi kutidalitsa.+Iye adzatikomera mtima,+ [Seʹlah.] Salimo 80:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Mulungu, tibwezeretseni mwakale.+Walitsani nkhope yanu kuti tipulumutsidwe.+
67 Mulungu adzatiyanja ndi kutidalitsa.+Iye adzatikomera mtima,+ [Seʹlah.] Salimo 80:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Mulungu, tibwezeretseni mwakale.+Walitsani nkhope yanu kuti tipulumutsidwe.+