Ekisodo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako iye anati: “Tsopano ngati mwandikomera mtima, inu Yehova, chonde, Yehova ayende nafe pakati pathu,+ chifukwa anthuwa ndi ouma khosi,+ ndipo mutikhululukire zolakwa zathu ndi machimo athu,+ ndi kutitenga kukhala chuma chanu.”+ Salimo 78:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma anawamvera chifundo.+ Anali kukhululukira* machimo awo+ ndipo sanali kuwawononga.+Nthawi zambiri anali kubweza mkwiyo wake,+Ndipo sanali kuwasonyeza ukali wake wonse.
9 Kenako iye anati: “Tsopano ngati mwandikomera mtima, inu Yehova, chonde, Yehova ayende nafe pakati pathu,+ chifukwa anthuwa ndi ouma khosi,+ ndipo mutikhululukire zolakwa zathu ndi machimo athu,+ ndi kutitenga kukhala chuma chanu.”+
38 Koma anawamvera chifundo.+ Anali kukhululukira* machimo awo+ ndipo sanali kuwawononga.+Nthawi zambiri anali kubweza mkwiyo wake,+Ndipo sanali kuwasonyeza ukali wake wonse.