Ekisodo 28:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno uike Urimu+ ndi Tumimu m’chovala pachifuwa chachiweruzo, ndipo zizikhala pamtima pa Aroni akamalowa kukaonekera pamaso pa Yehova. Aroni azinyamula ziweruzo+ za ana a Isiraeli pamtima pake poonekera kwa Yehova nthawi zonse. Levitiko 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anamuveka chovala cha pachifuwa+ ndi kuika Urimu ndi Tumimu+ m’chovala cha pachifuwacho. Ezara 2:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Pa chifukwa chimenechi, Tirisata*+ anawauza kuti sayenera kudya+ zinthu zopatulika koposa, kufikira patakhala wansembe wokhala ndi Urimu+ ndi Tumimu.
30 Ndiyeno uike Urimu+ ndi Tumimu m’chovala pachifuwa chachiweruzo, ndipo zizikhala pamtima pa Aroni akamalowa kukaonekera pamaso pa Yehova. Aroni azinyamula ziweruzo+ za ana a Isiraeli pamtima pake poonekera kwa Yehova nthawi zonse.
63 Pa chifukwa chimenechi, Tirisata*+ anawauza kuti sayenera kudya+ zinthu zopatulika koposa, kufikira patakhala wansembe wokhala ndi Urimu+ ndi Tumimu.