Deuteronomo 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako. Deuteronomo 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+
25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako.
3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+